9 Komanso Uziya anamanga nsanja+ ku Yerusalemu pafupi ndi Geti la Pakona,+ Geti la Kuchigwa+ ndiponso pafupi ndi Mchirikizo wa Khoma ndipo nsanjazo anazilimbitsa.
24 Binui mwana wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika pamene panali khoma lothandizira kuti mpanda usagwe+ mpaka pakona ya mpanda wa mzindawo.