Nehemiya 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako, Binui mwana wamwamuna wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika ku Mchirikizo wa Khoma+ ndi kukona ya mpanda wa mzindawo.
24 Kenako, Binui mwana wamwamuna wa Henadadi anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera panyumba ya Azariya kukafika ku Mchirikizo wa Khoma+ ndi kukona ya mpanda wa mzindawo.