Genesis 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adamu ali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Seti.+ Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+
3 Adamu ali ndi zaka 130, anabereka mwana wamwamuna wofanana naye ndipo anamʼpatsa dzina lakuti Seti.+
5 Taonani! Ndinabadwa ndili wochimwa,Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+