Yobu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi munthu wochimwa angabereke munthu wosachimwa?*+ Ayi nʼzosatheka. Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Popeza anthu onse ndi ochimwa ndipo amalephera kusonyeza bwinobwino ulemerero wa Mulungu.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+
12 Uchimo unalowa mʼdziko kudzera mwa munthu mmodzi ndipo uchimowo unabweretsa imfa.+ Choncho imfayo inafalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa . . .+