-
Mlaliki 9:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse+ komanso salandira mphoto iliyonse,* chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zimaiwalika.+ 6 Komanso chikondi chawo, chidani chawo ndi nsanje yawo zatha kale, ndipo alibenso gawo lililonse pa zimene zikuchitika padziko lapansi pano.+
-