Salimo 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, agululeni mano mʼkamwa mwawo. Inu Yehova, thyolani nsagwada za mikango* imeneyi. Miyambo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pali mʼbadwo umene mano ake ndi malupangaNdiponso umene nsagwada zake ndi mipeni yophera nyama.Mʼbadwowo umapondereza anthu ovutika apadziko lapansiKomanso osauka pakati pa anthu.+
14 Pali mʼbadwo umene mano ake ndi malupangaNdiponso umene nsagwada zake ndi mipeni yophera nyama.Mʼbadwowo umapondereza anthu ovutika apadziko lapansiKomanso osauka pakati pa anthu.+