Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kodi palibe aliyense womvetsa zinthu pakati pa anthu ochita zoipawa?

      Iwo amadya anthu anga ngati kuti akudya chakudya.

      Ndipo sapemphera kwa Yehova.

  • Miyambo 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Amene amabera mwachinyengo munthu wosauka kuti awonjezere chuma chake+

      Komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera,

      Ndithu adzasauka.

  • Yesaya 32:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Munthu wamakhalidwe oipa, njira zake nʼzoipa.+

      Iye amalimbikitsa anthu kuchita khalidwe lochititsa manyazi

      Nʼcholinga choti asokoneze munthu wozunzika ndi wosauka pogwiritsa ntchito mabodza,+

      Ngakhale pamene munthuyo akunena zoona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena