-
2 Mafumu 22:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Nʼchifukwa chake ndidzakuika mʼmanda a makolo ako ndipo udzaikidwa mʼmanda ako mwamtendere. Maso ako sadzaona tsoka lonse limene ndidzabweretse pamalo ano.’”’” Kenako iwo anakauza mfumuyo zimenezi.
-