Mlaliki 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndi mapeto a munthu aliyense, ndipo amene ali ndi moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.
2 Ndi bwino kupita kunyumba yamaliro kusiyana ndi kupita kunyumba yamadyerero,+ chifukwa amenewo ndi mapeto a munthu aliyense, ndipo amene ali ndi moyo aziganizira zimenezi mumtima mwake.