Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Uziti ukalima nthaka, suzikolola mokwanira. Udzakhala moyo woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi.”

  • Salimo 109:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ana ake* aziyendayenda ndipo akhale opemphapempha.

      Azichoka mʼmabwinja mmene akukhala, nʼkukafunafuna chakudya.

  • Danieli 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Inuyo adzakuthamangitsani pakati pa anthu ndipo muzidzakhala ndi nyama zakutchire. Muzidzadya udzu ngati ngʼombe ndipo muzidzanyowa ndi mame akumwamba.+ Ndiyeno padzadutsa+ nthawi zokwana 7+ mpaka mutadziwa kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu ndiponso kuti amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena