Genesis 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno ana a Mulungu woona*+ anayamba kuona kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Choncho anayamba kutenga akazi alionse amene ankawafuna nʼkuwakwatira. Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+ Yobu 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene nyenyezi zamʼmawa+ zinafuula pamodzi mosangalala,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu*+ anayamba kufuula mosangalala?
2 Ndiyeno ana a Mulungu woona*+ anayamba kuona kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Choncho anayamba kutenga akazi alionse amene ankawafuna nʼkuwakwatira.
2 Iye anati: “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri. Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+
7 Pamene nyenyezi zamʼmawa+ zinafuula pamodzi mosangalala,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu*+ anayamba kufuula mosangalala?