Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno ana a Mulungu woona*+ anayamba kuona kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Choncho anayamba kutenga akazi alionse amene ankawafuna nʼkuwakwatira.

  • 1 Mafumu 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+

  • Yobu 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano linafika tsiku limene ana a Mulungu woona*+ anapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo Satana+ nayenso anafika pakati pawo.+

  • Yobu 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pambuyo pa zimenezi, linafika tsiku limene ana a Mulungu woona*+ anapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo Satana nayenso anapita kukaonekera pamaso pa Yehova.+

  • Salimo 89:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndi ndani kumwamba amene angafanane ndi Yehova?+

      Ndi ndani pakati pa ana a Mulungu+ amene ndi wofanana ndi Yehova?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena