Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo ngati chovala.Chilungamo changa chinali ngati mkanjo* komanso nduwira.