Yobu 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*
14 Ndinkavala chilungamo, ndipo icho chinkandiveka.+Chilungamo changa chinali ngati malaya akunja odula manja, ndi nduwira.*