Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 45:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Tsoka kwa amene akulimbana* ndi amene anamupanga,

      Chifukwa iye ali ngati phale

      Limene lili pakati pa mapale ena amene ali pansi.

      Kodi dongo lingafunse woumba mbiya* kuti: “Kodi ukupanga chiyani?”+

      Kapena kodi chinthu chimene unapanga chinganene kuti: “Amene uja alibe manja”?*

  • Aroma 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu iwe, ndiwe ndani kuti uziyankhana ndi Mulungu?+ Kodi chinthu choumbidwa chingauze munthu amene anachiumba kuti, “Unandipangiranji chonchi?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena