2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+ Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah) Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ Luka 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mwanayo anauza bambo akewo kuti, ‘Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+ Si inenso woyenera kutchulidwa kuti mwana wanu.’ 1 Yohane 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, choncho tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira komanso kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+
13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
21 Ndiyeno mwanayo anauza bambo akewo kuti, ‘Bambo, ndachimwira kumwamba komanso ndachimwira inu.+ Si inenso woyenera kutchulidwa kuti mwana wanu.’
9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, choncho tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira komanso kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+