Salimo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mawu apakamwa panga komanso zimene ndimaganizira mozama mumtima mwanga,Zizikusangalatsani, inu Yehova,+ Thanthwe langa+ ndiponso Wondiwombola.+ Yesaya 38:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+
14 Mawu apakamwa panga komanso zimene ndimaganizira mozama mumtima mwanga,Zizikusangalatsani, inu Yehova,+ Thanthwe langa+ ndiponso Wondiwombola.+
17 Mʼmalo mopeza mtendere ndinali ndi chisoni chachikulu.Koma chifukwa chakuti mumandikonda kwambiri,Munanditeteza kuti ndisapite kudzenje lachiwonongeko.+ Machimo anga onse mwawaponyera kumbuyo kwanu.*+