Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndikunena zoona, mawu anga si onama.

      Amene amadziwa chilichonse+ akukuonani.

  • Salimo 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+

      Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+

      Iye ndi chishango kwa anthu onse amene amathawira kwa iye.+

  • Salimo 104:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+

      Zonsezo munazipanga mwanzeru.+

      Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena