Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+

      Njira zake zonse ndi zolungama.+

      Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+

      Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+

  • Danieli 4:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Tsopano ine Nebukadinezara ndikutamanda, kukweza ndi kulemekeza Mfumu yakumwamba,+ chifukwa ntchito zake zonse ndi zogwirizana ndi choonadi, njira zake ndi zolungama+ ndiponso amatha kutsitsa anthu onyada.”+

  • Chivumbulutso 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti:

      “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena