Genesis 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+ Salimo 77:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Koma palibe amene anatha kuzindikira mmene mapazi anu anaponda.
2 Dziko lapansi linali lopanda chilichonse. Padzikoli panali madzi ambiri+ ndipo pamwamba pake panali mdima wokhawokha. Mphamvu ya Mulungu+ inkayendayenda* pamwamba pa madziwo.+
19 Msewu wanu unadutsa panyanja,+Ndipo njira yanu inadutsa pamadzi ambiri.Koma palibe amene anatha kuzindikira mmene mapazi anu anaponda.