Salimo 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Bwerani mwamsanga mudzandithandize,Inu Yehova, amene mumandipulumutsa.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Chivumbulutso 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anapitiriza kufuula ndi mawu okweza akuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu, amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
10 Iwo anapitiriza kufuula ndi mawu okweza akuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu, amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+