1 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsikuli, mmodzi wa atumiki a Sauli anali kumeneko chifukwa anali atamusunga pamaso pa Yehova. Dzina lake anali Doegi+ ndipo anali wa ku Edomu.+ Iye anali mkulu wa abusa a Sauli. Salimo 94:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+ 4 Zolankhula zawo zimasonyeza kuti ndi opusa komanso onyada.Anthu onse ochita zoipa amalankhula modzitama.
7 Pa tsikuli, mmodzi wa atumiki a Sauli anali kumeneko chifukwa anali atamusunga pamaso pa Yehova. Dzina lake anali Doegi+ ndipo anali wa ku Edomu.+ Iye anali mkulu wa abusa a Sauli.
3 Inu Yehova, kodi anthu oipa adzapitiriza kusangalala mpaka liti?Adzapitiriza kukondwera mpaka liti?+ 4 Zolankhula zawo zimasonyeza kuti ndi opusa komanso onyada.Anthu onse ochita zoipa amalankhula modzitama.