Miyambo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+ Miyambo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mboni yonama sidzalephera kulangidwa,Ndipo amene amalankhula zabodza zokhazokha adzawonongedwa.+
19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+