Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+ Aroma 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse apatuka, ndipo onse akhala opanda pake. Palibiretu ndi mmodzi yemwe amene akusonyeza kukoma mtima.”+
20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+
12 Anthu onse apatuka, ndipo onse akhala opanda pake. Palibiretu ndi mmodzi yemwe amene akusonyeza kukoma mtima.”+