2 Mbiri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+ Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayangʼana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+ 2 Akorinto 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anatipulumutsa ku zinthu zimenezi zomwe zikanatha kutipha ndipo adzatipulumutsanso. Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+
12 Inu Mulungu wathu kodi simuwaweruza?+ Ifeyo tilibe mphamvu zotha kulimbana ndi gulu lalikulu limene likudzamenyana nafeli ndipo sitikudziwa chochita,+ koma maso athu ali pa inu.”+
15 Maso anga amayangʼana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+
10 Iye anatipulumutsa ku zinthu zimenezi zomwe zikanatha kutipha ndipo adzatipulumutsanso. Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+