18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse ndipo adzandisunga kuti ndikakhale mu Ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+