Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chifukwa palibe amene angakhulupirire chilichonse chimene anena.

      Mʼmitima yawo muli chidani chokhachokha.

      Mmero wawo ndi manda otseguka.

      Iwo amalankhula zachinyengo* ndi lilime lawo.+

  • Salimo 28:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa, amene amachita zopweteka anzawo,+

      Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo, koma mʼmitima yawo muli zinthu zoipa.+

  • Salimo 55:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta amumkaka,+

      Koma mumtima mwake amakonda nkhondo.

      Mawu ake ndi osalala kuposa mafuta,

      Koma ali ngati malupanga akuthwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena