Salimo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+
9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+Mmero wawo ndi manda otseguka.+Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+