Salimo 62:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ndithudi, ndikuyembekezera* Mulungu modekha. Chipulumutso changa chimachokera kwa iye.+ 2 Iye ndi thanthwe langa komanso ndi amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.*+Sindidzagwedezeka kwambiri.+ Salimo 71:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa chiyembekezo changa ndi inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.Ndakhala ndikudalira inu kuyambira ndili mnyamata.+
62 Ndithudi, ndikuyembekezera* Mulungu modekha. Chipulumutso changa chimachokera kwa iye.+ 2 Iye ndi thanthwe langa komanso ndi amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.*+Sindidzagwedezeka kwambiri.+
5 Chifukwa chiyembekezo changa ndi inu Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.Ndakhala ndikudalira inu kuyambira ndili mnyamata.+