Salimo 37:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya mavuto.+ Salimo 68:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atamandike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona amene amatipulumutsa. (Selah) Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya mavuto.+
19 Atamandike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+Mulungu woona amene amatipulumutsa. (Selah)
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+