1 Samueli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Munthune ndili ndi nkhawa kwambiri. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa, koma ndikufotokozera Yehova nkhawa zanga zonse.+
15 Koma Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Munthune ndili ndi nkhawa kwambiri. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa chilichonse choledzeretsa, koma ndikufotokozera Yehova nkhawa zanga zonse.+