Salimo 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu wanga, ine ndataya mtima.+ Nʼchifukwa chake ndakukumbukirani,+Pamene ndili mʼdziko la Yorodano ndi mʼmapiri a Herimoni,Pamene ndili mʼPhiri la Mizara.* Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Muzimudalira nthawi zonse, anthu inu. Mukhuthulireni zonse zamumtima mwanu.+ Mulungu ndi malo athu othawirako.+ (Selah) Salimo 142:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimakhuthula nkhawa zanga pamaso pake.Ndimafotokoza mavuto anga pamaso pake+
6 Inu Mulungu wanga, ine ndataya mtima.+ Nʼchifukwa chake ndakukumbukirani,+Pamene ndili mʼdziko la Yorodano ndi mʼmapiri a Herimoni,Pamene ndili mʼPhiri la Mizara.*
8 Muzimudalira nthawi zonse, anthu inu. Mukhuthulireni zonse zamumtima mwanu.+ Mulungu ndi malo athu othawirako.+ (Selah)