Miyambo 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu woipa amakodwa ndi zolankhula zake zochimwa,+Koma wolungama amapulumuka pamavuto. Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa mʼpamene pamamuchititsa kuti awonongedwe,+Ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.
7 Pakamwa pa munthu wopusa mʼpamene pamamuchititsa kuti awonongedwe,+Ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.