Deuteronomo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ndi amene muyenera kumutamanda.+ Iyeyo ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha zonsezi, zimene mwaziona ndi maso anu.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
21 Iye ndi amene muyenera kumutamanda.+ Iyeyo ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha zonsezi, zimene mwaziona ndi maso anu.+
3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+