Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 145:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova ndi wolungama mʼnjira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika pa chilichonse chimene amachita.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
17 Yehova ndi wolungama mʼnjira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika pa chilichonse chimene amachita.+