-
Deuteronomo 11:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma dziko limene mwatsala pangʼono kuwolokerako nʼkukalitenga kuti likhale lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Limamwa madzi a mvula amene amagwa kuchokera kumwamba.+ 12 Limeneli ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kumayambiriro kwa chaka mpaka kumapeto.
-