Salimo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa iye sananyoze kapena kunyansidwa ndi kuvutika kwa munthu woponderezedwa.+Sanabise nkhope yake kwa iye.+ Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+
24 Chifukwa iye sananyoze kapena kunyansidwa ndi kuvutika kwa munthu woponderezedwa.+Sanabise nkhope yake kwa iye.+ Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+