Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa. Salimo 102:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandibisire nkhope yanu pamene ndili pamavuto aakulu.+ Tcherani khutu lanu kwa ine.*Ndiyankheni mofulumira pamene ndikuitana.+
9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa.
2 Musandibisire nkhope yanu pamene ndili pamavuto aakulu.+ Tcherani khutu lanu kwa ine.*Ndiyankheni mofulumira pamene ndikuitana.+