Salimo 69:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo musabise nkhope yanu kwa mtumiki wanu.+ Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndili pamavuto aakulu.+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyankheni mofulumira, inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.*+ Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
17 Ndipo musabise nkhope yanu kwa mtumiki wanu.+ Ndiyankheni mwamsanga, chifukwa ndili pamavuto aakulu.+
7 Ndiyankheni mofulumira, inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.*+ Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+