Mlaliki 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa moyo wanga wopanda pakewu,+ ndaona chilichonse. Ndaona munthu wolungama amene amawonongeka akuchita zinthu zolungama,+ komanso ndaona munthu woipa amene amakhala ndi moyo wautali ngakhale kuti akuchita zoipa.+
15 Pa moyo wanga wopanda pakewu,+ ndaona chilichonse. Ndaona munthu wolungama amene amawonongeka akuchita zinthu zolungama,+ komanso ndaona munthu woipa amene amakhala ndi moyo wautali ngakhale kuti akuchita zoipa.+