Deuteronomo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndi amene anakutengani nʼkukutulutsani mungʼanjo yosungunulira zitsulo, anakutulutsani mu Iguputo, kuti mukhale anthu ake,*+ monga mmene mulili lero. Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+
20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndi amene anakutengani nʼkukutulutsani mungʼanjo yosungunulira zitsulo, anakutulutsani mu Iguputo, kuti mukhale anthu ake,*+ monga mmene mulili lero.