Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Dzukani. Nʼchifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+ Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+ Yesaya 64:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poona zinthu zonsezi, kodi mupitiriza kumangokhala osachitapo kanthu, inu Yehova? Kodi mungokhala chete nʼkumaonerera ife tikusautsidwa koopsa?+ Maliro 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye wathetsa mphamvu zonse za* Isiraeli atakwiya kwambiri. Adani athu atatiukira, iye sanatithandize,+Ndipo mkwiyo wakewo unapitiriza kuyakira Yakobo ngati moto umene wawononga chilichonse chimene chili pafupi.+
12 Poona zinthu zonsezi, kodi mupitiriza kumangokhala osachitapo kanthu, inu Yehova? Kodi mungokhala chete nʼkumaonerera ife tikusautsidwa koopsa?+
3 Iye wathetsa mphamvu zonse za* Isiraeli atakwiya kwambiri. Adani athu atatiukira, iye sanatithandize,+Ndipo mkwiyo wakewo unapitiriza kuyakira Yakobo ngati moto umene wawononga chilichonse chimene chili pafupi.+