Salimo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+ Salimo 78:65, 66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Kenako Yehova anadzuka ngati kuti anali mtulo,+Ngati mmene amadzukira munthu wamphamvu+ pambuyo pomwa vinyo wambiri. 66 Iye anathamangitsa adani ake nʼkuwabweza,+Anachititsa kuti adaniwo akhale onyozeka mpaka kalekale.
6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+
65 Kenako Yehova anadzuka ngati kuti anali mtulo,+Ngati mmene amadzukira munthu wamphamvu+ pambuyo pomwa vinyo wambiri. 66 Iye anathamangitsa adani ake nʼkuwabweza,+Anachititsa kuti adaniwo akhale onyozeka mpaka kalekale.