Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+
2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+ Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+
22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+