Salimo 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu Mulungu, ndinu Mfumu yanga.+Lamulani kuti Yakobo apambane.* Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala Mfumu!+ Dziko lapansi lisangalale.+ Zilumba zambiri zikondwere.+ Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga lake.+ Ndiyeno kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala Ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake+ ndipo iye adzalamulira monga mfumu mpaka kalekale.”+
17 Iwo ankanena kuti: “Tikukuthokozani inu Yehova,* Mulungu Wamphamvuyonse, inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu zanu zazikulu nʼkuyamba kulamulira monga mfumu.+