Machitidwe 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa zonse zimene anawalonjezazo kwa ife ana awo poukitsa Yesu,+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti: ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako.’+ Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+ Aheberi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ podziika yekha kukhala mkulu wa ansembe. Koma amene anamupatsa ulemerero umenewo ndi amene anamuuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako.”+
33 Uthengawo ndi wakuti Mulungu wakwaniritsa zonse zimene anawalonjezazo kwa ife ana awo poukitsa Yesu,+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mu salimo lachiwiri kuti: ‘Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako.’+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako”?+ Komanso kuti: “Ine ndidzakhala bambo ake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
5 Zilinso chimodzimodzi ndi Khristu. Iye sanadzipatse yekha ulemerero+ podziika yekha kukhala mkulu wa ansembe. Koma amene anamupatsa ulemerero umenewo ndi amene anamuuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala bambo ako.”+