Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+ 2 Samueli 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lapansi linayamba kugwedezeka ndiponso kunjenjemera;+Maziko akumwamba anagwedezeka.+Anagwedezeka chifukwa Mulungu anakwiya.+
18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+
8 Dziko lapansi linayamba kugwedezeka ndiponso kunjenjemera;+Maziko akumwamba anagwedezeka.+Anagwedezeka chifukwa Mulungu anakwiya.+