Ekisodo 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aisiraeliwo ankauza Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera mʼdziko la Iguputo, kumene tinkadya nyama+ ndi mkate nʼkukhuta. Mʼmalomwake mwatibweretsa mʼchipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+
3 Aisiraeliwo ankauza Mose ndi Aroni kuti: “Zikanakhala bwino dzanja la Yehova likanatiphera mʼdziko la Iguputo, kumene tinkadya nyama+ ndi mkate nʼkukhuta. Mʼmalomwake mwatibweretsa mʼchipululu muno kuti muphetse mpingo wonsewu ndi njala.”+