Salimo 103:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tamandani Yehova, inu angelo ake onse+ amphamvu,Amene amamvera mawu ake komanso kuchita zimene wanena.+
20 Tamandani Yehova, inu angelo ake onse+ amphamvu,Amene amamvera mawu ake komanso kuchita zimene wanena.+