Numeri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mose anamva anthu akulira mʼbanja lililonse, munthu aliyense pakhomo la tenti yake. Ndipo Yehova anakwiya kwambiri+ komanso Mose anakhumudwa kwambiri.
10 Mose anamva anthu akulira mʼbanja lililonse, munthu aliyense pakhomo la tenti yake. Ndipo Yehova anakwiya kwambiri+ komanso Mose anakhumudwa kwambiri.